Genesis 49:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Benjamini ali ngati mmbulu wolusa umene m'maŵa umapha ndi kudya zimene udagwira, ndipo madzulo umagaŵa zimene udagwirazo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Benjamini ndiye mmbulu wakulusalusa; m'mamawa adzadya chomotola, madzulo adzagawa zofunkha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Benjamini ali ngati mʼmbulu wolusa; umene mmawa umapha ndi kudya zofunkha, ndipo madzulo umagawa zofunkhazo,”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Benjamini ndiye mmbulu wakulusalusa; M'mamawa adzadya comotola, Madzulo adzagawa zofunkha.