Genesis 49:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Uli ngati chigumula cha madzi oopsa, koma sudzakhalanso wopambana, chifukwa chakuti sudaope kugona pa bedi la ine bambo wako. Udaloŵa m'bedi langa, nuliipitsa!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wobwabwada ngati madzi; sudzapambana; chifukwa unakwera pa kama wa atate wako; pamenepo unaipitsapo; anakwera paja ndigonapo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wokokoma ngati madzi a chigumula, koma sudzakhalanso wopambana, iwe unagona pa bedi la abambo ako, ndithu unayipitsa bedi la mdzakazi wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wobwabwada ngati madzi; sudzapambana; Cifukwa unakwera pa kama wa atate wako; Pamenepo unaipitsapo; anakwera paja ndigonapo.