Genesis 49:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Simeoni ndi Levi mpachibale pao, amagwiritsa ntchito zida zankhondo pochita chiwawa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Simeoni ndi Levi ndiwo abale; zida za mphulupulu ndizo malupanga ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Simeoni ndi Levi ndi pachibale pawo, anachitira nkhanza anthu amene anachita nawo pangano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Simeoni ndi Levi ndiwo abale; Zida za mphulupulu ndizo malupanga ao.