Genesis 5:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamwalira ali wa zaka 910.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
masiku ake onse a Kenani anali zaka mazana asanu ndi anai kudza khumi; ndipo anamwalira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zaka zonse za Kenani zinali 910, ndipo anamwalira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
masiku ace onse a Kenani anali zaka mazana asanu ndi anai kudza khumi; ndipo anamwalira.