Genesis 5:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo adakhalanso ndi moyo zaka zina 830. Adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo Mahalalele anakhala ndi moyo, atabala Yaredi, zaka mazana asanu ndi atatu kudza makumi atatu, nabala ana aamuna ndi aakazi:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atabadwa Yaredi, Mahalaleli anakhala ndi moyo zaka zina 830 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo Mahalalele anakhala ndi moyo, atabala Yaredi, zaka mazana asanu ndi atatu kudza makumi atatu, nabala ana amuna ndi akazi: