Genesis 5:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yaredi ali wa zaka 162, adabereka mwana dzina lake Enoki,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yaredi anakhala ndi moyo zaka zana kudza makumi asanu ndi limodzi ndi ziwiri, nabala Enoki;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Yaredi anali ndi zaka 162, anabereka Enoki.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yaredi anakhala ndi moyo zaka zana kudza makumi asanu ndi limodzi ndi ziwiri, nabala Enoke;