Genesis 5:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamwalira ali wa zaka 962.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
masiku ake onse a Yaredi anali zaka mazana asanu ndi anai kudza makumi asanu ndi limodzi ndi ziwiri: ndipo anamwalira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zaka zonse za Yaredi zinali 962 ndipo anamwalira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
masiku ace onse a Yaledi anali zaka mazana asanu ndi anai kudza maitumi asanu ndi limodzi ndi ziwiri: ndipo anamwalira.