Genesis 5:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Enoki ali wa zaka 65, adabereka mwana dzina lake Metusela.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Enoki anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi limodzi kudza zisanu, nabala Metusela:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Enoki anali ndi zaka 65, anabereka Metusela.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Enoke anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi limodzi kudza zisanu, nabala Metusela: