Genesis 5:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamwalira ali wa zaka 365.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
masiku ake onse a Enoki anali mazana atatu kudza makumi asanu ndi limodzi ndi zisanu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zaka zonse za Enoki zinali 365.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
masiku ace onse a Enoke anali mazana atatu kudza makumi asanu ndi limodzi ndi zisanu;