Genesis 5:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Metusela ali wa zaka 187, adabereka mwana dzina lake Lameki,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Metusela anakhala ndi moyo zaka zana kudza makumi asanu ndi atatu ndi zisanu ndi ziwiri, nabala Lameki;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Metusela anali ndi zaka 187, anabereka Lameki.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Metusela anakhala ndi moyo zaka zana kudza makumi asanu ndi atatu ndi zisanu ndi ziwiri, nabala Lameke;