Genesis 5:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Lameki ali wa zaka 182, adabereka mwana,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Lameki anakhala ndi moyo zaka zana kudza makumi asanu ndi atatu ndi ziwiri, nabala mwana wamwamuna;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Lameki anali ndi zaka 182, anabereka mwana wamwamuna.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Lameke anakhala ndi moyo zaka zana kudza makumi asanu ndi atatu ndi ziwiri, nabala mwana wamwamuna;