Genesis 5:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamu ali wa zaka 130 adabereka mwana wofanafana ndi iye, namutcha Seti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Adamu anakhala ndi moyo zaka zana limodzi kudza makumi atatu, nabala mwana wamwamuna m'chifanizo chake; namutcha dzina lake Seti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Adamu anali ndi zaka 130, anabereka mwana wamwamuna wofanana naye ndipo anamutcha Seti.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Adamu anakhala ndi moyo zaka zana limodzi kudza makumi atatu, nabala mwana wamwamuna m'cifanizo cace; namucha dzina lace Seti.