Genesis 5:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamwalira ali wa zaka 777.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
masiku ake onse a Lameki anali zaka mazana asanu ndi awiri kudza makumi asanu ndi awiri; ndipo anamwalira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zaka zonse za Lameki zinali 777, ndipo kenaka anamwalira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
masiku ace onse a Lameke anali zaka mazana asanu ndi awiri kudza makumi asanu ndi awiri; ndipo anamwa lira.