Genesis 5:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Seti ali wa zaka 105, adabereka mwana dzina lake Enosi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Seti anakhala ndi moyo zaka zana kudza zisanu, nabala Enosi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Seti anali ndi zaka 105, anabereka Enosi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Seti anakhala ndi moyo zaka zana kudza zisanu, nabala Enosi;