Genesis 50:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Yakobe adachitadi monga momwe bambo wao adaaŵalamulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana ake amuna anamchitira iye monga anawalamulira iwo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho ana a Yakobo anachita monga momwe abambo awo anawalamula:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana ace amuna anamcitira iye monga anawalamulira iwo;