Genesis 50:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adauza abale ake aja kuti, “Patsala pang'ono kuti ndikusiyeni, koma Mulungu adzakusungani ndithu, ndipo adzakutulutsani m'dziko muno, kupita nanu ku dziko limene adaalonjeza Abrahamu, Isaki ndi Yakobe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yosefe ndipo anati kwa abale ake, Ndilinkufa ine, koma Mulungu adzaonekera kwa inu, adzakuchotsani inu m'dziko muno kubwera kunka ku dziko limene analumbirira kwa Abrahamu ndi kwa Isaki, ndi kwa Yakobo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Yosefe anati kwa abale ake, “Ine ndatsala pangʼono kufa. Koma mosakayika Mulungu adzakuyangʼanirani nadzakutengani kukutulutsani mʼdziko lino kupita ku dziko limene Iye analonjeza kwa Abrahamu, Isake ndi Yakobo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yosefe ndipo anati kwa abale ace, Ndirinkufa ine, koma Mulungu adzaonekera kwa inu, adzakucotsani inu m'dziko muno kubwera kunka ku dziko limene analumbirira kwa Abrahamu ndi kwa Isake, ndi kwa Yakobo