Genesis 50:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yosefe atatha kulira maliro a bambo wake, adauza nduna za Farao kuti, “Chonde mundikomere mtima, Farao mukamuuze kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atapita masiku akumlira iye, Yosefe anati kwa mbumba ya Farao, kuti, Ngatitu ndapeza ufulu pamaso panu, nenanitu m'makutu a Farao kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yosefe atatha kulira maliro a abambo ake, anayankhula kwa nduna za Farao nati, “Ngati mungandikomere mtima, chonde mundiyankhulire kwa Farao kumuwuza kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atapita masiku akumlira iye Yosefe anati kwa mbumba ya Farao kuti, Ngatitu ndapeza ufulu pamase panu, nenanitu m'makutu a Parae kuti,