Genesis 50:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
‘Pamene bambo wanga anali pafupi kufa, adandilumbiritsa kuti ndikamuike m'manda amene adadzikumbira m'dziko la Kanani. Motero chonde, mundilole kuti ndipite ndikaike bambo wanga, pambuyo pake ndidzabweranso.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atate wanga anandilumbiritsa ine, kuti, Taona, ndilinkufa; m'manda m'mene ndadzikonzeratu ndekha m'dziko la Kanani, m'menemo udzandiika ine. Tsopano mundiloletu, ndikwereko, ndipite, ndikaike atate wanga, nditatero ndidzabweranso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
‘Abambo anga anandilumbiritsa ndipo anati, ‘Ndatsala pangʼono kumwalira, ukandiyike mʼmanda amene ndinakumba ndekha mʼdziko la Kanaani.’ Tsono mundilole ndikayike abambo anga, ndipo ndikabweranso.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atate wanga anandilumbi ritsa ine, kuti, Taona, ndirinkufa m'manda m'mene ndadzikonzeran ndekha m'dziko la Kanani, m'menemo udzandiika ine. Tsopano mundi loletu, ndikwereko, ndipite, ndikaike atate wanga, nditatero ndidzabwe ranso.