Genesis 6:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi imeneyo anthu anali atayamba kuchuluka pa dziko lonse lapansi, ndipo adabereka ana aakazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali pamene anthu anayamba kuchuluka padziko, ndi ana akazi anawabadwira iwo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu atayamba kuchuluka pa dziko lapansi ndi kubereka ana aakazi,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali pamene anthu anayamba kucuruka padziko, ndi ana akazi anawabadwira iwo,