Genesis 6:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'litali mwake mwa chombocho mukhale mamita 140. M'mimba mwake mukhale mamita 23, ndipo msinkhu wake ukhale wa mamita 13 ndi theka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kupanga kwake ndi kotere: m'litali mwake mwa chingalawa mikono mazana atatu, m'mimba mwake mikono makumi asanu, m'msinkhu mwake mikono makumi atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uchipange motere: Chombo chikhale mamita 140 mulitali, mamita 23 mulifupi ndi mamita 13 mu msinkhu wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kupanga kwace ndi kotere: m'litari mwace mwa cingalawa mikono mazana atatu, m'mimba mwace mikono makumi asanu, m'msinkhu mwace mikono makumi atatu.