Genesis 8:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atadikira masiku asanu ndi aŵiri ena, adaitulutsanso nkhunda ija m'chombo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo analinda masiku ena asanu ndi awiri; natulutsanso njiwayo m'chingalawamo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho anadikirabe masiku ena asanu ndi awiri ndipo anatulutsanso nkhundayo mʼchombo muja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo analinda masiku ena asanu ndi awiri; naturutsanso njiwayo m'cingalawamo;