Genesis 8:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe ndi mkazi wako, ana ako pamodzi ndi akazi ao, tulukani m'chombomo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tulukamoni m'chingalawamo, iwe ndi ana ako, ndi mkazi wako, ndi akazi a ana ako pamodzi ndi iwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwe, mkazi wako, ana ako pamodzi ndi akazi awo tulukani mʼchombomo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Turukamoni m'cingalawamo, iwe ndi ana ako, ndi mkazi wako, ndi akazi a ana ako pamodzi ndi iwe.