Genesis 8:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nyama zonse, zokwaŵa zonse, mbalame zonse, ndi zina zonse zoyenda pansi pano zidatuluka m'chombomo m'magulumagulu potsata mitundu yake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
zinyama zonse, zokwawa zonse, zouluka zonse, ndi zonse zokwawa pa dziko lapansi, monga mwa mitundu yao, zinatuluka m'chingalawamo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyama zonse, zokwawa zonse, mbalame zonse, chilichonse choyenda pa dziko lapansi, zinatuluka mʼchombo motsogozana monga mwa mitundu yawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
zinyama zonse, zokwawa zonse, zouluka zonse, ndi zonse zokwawa pa dziko lapansi, monga mwa mitundu yao, zinaturuka m'cingalawamo.