Genesis 8:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akasupe a madzi ambiri okhala pansi pa dziko pamodzi ndi zipata zakuthambo, adazitseka. Mvula adailetsa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo anatsekedwa akasupe a madzi aakulu ndi mazenera a kumwamba, niletsedwa mvula ya kumwamba;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono akasupe a madzi ambiri a pansi pa dziko ndi zitseko za madzi a kumwamba zinatsekedwa, ndipo mvula inaleka kugwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo anatsekedwa akasupe a madzi akuru ndi mazenera a kumwamba, niletsedwa mvula ya kwuwamba;