Genesis 8:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo madzi adayamba kutsika pang'onopang'ono. Masiku 150 atapita, madziwo anali atatsika ndithu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo madzi anaphweraphwerabe pa dziko lapansi: pamene anatha masiku zana limodzi kudza makumi atatu madzi anachepa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Madzi amaphwabe pa dziko lapansi. Pakutha pa masiku 150, madzi anatsika,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo madzi anaphweraphwerabe pa dziko lapansi: pamene anatha masiku zana limodzi kudza makumi atatu madzi anacepa.