Genesis 8:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
natulutsa khwangwala. Khwangwalayo ankangouluka mu mlengalenga kudikira kuti madzi aphwe pa dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo anatulutsa khungubwi, ndipo anatuluka kunka kwina ndi kwina kufikira adaphwa madzi pa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
natulutsa khwangwala, koma khwangwalayo ankangowuluka uku ndi uku mpaka madzi anawuma pa dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo anaturutsa khungubwe, ndipo anaturuka kunka kwina ndi kwina kufikira adaphwa madzi pa dziko lapansi,