Habakkuk 1:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka amapitirira mofulumira ngati mphepo. Anthuwo amene mphamvu ndiye mulungu wao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo adzapitirira ngati mphepo, nadzalakwa ndi kupalamula, iye amene aiyesa mphamvu yake mulungu wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka amasesa mofulumira ngati mphepo nʼkumangopitirirabe, anthu ochimwa, amene mphamvu zawo ndiye mulungu wawo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo adzapitirira ngati mphepo, oadzalakwa ndi kuparamula, iye amene aiyesa mphamvu yace mulungu wace.