Habakkuk 1:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adani ao amachita ngati kuŵedza anthuwo ndi mbedza, kapena kuŵakola m'kombe. Amaŵakokera m'matchera ao, ndipo amakondwa ndi kusangalala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Aziwedza zonse ndi mbedza, azigwira m'ukonde wake, nazisonkhanitsa m'khoka mwake; chifukwa chake asekera nakondwerera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mdani wawo woyipa amakoka anthu onse ndi mbedza, amawakola mu ukonde wake, amawasonkhanitsa mu khoka lake; kotero iyeyo amakondwa ndi kusangalala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Aziwedza zonse ndi mbedza, azigwira m'ukonde wace, nazisonkhanitsa m'khoka mwace; cifukwa cace asekera nakondwerera.