Habakkuk 1:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi adzapitirirabe kugwiritsa ntchito makoka ao, ndi kumapha mitundu ya anthu mopanda chifundo mpakampaka?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi m'mwemo adzakhuthula m'ukonde mwake osaleka kuphabe amitundu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi iye azipitirabe kugwiritsa ntchito makoka akewo, kuwononga mitundu ya anthu mopanda chifundo?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi m'mwemo adzakhuthula m'ukonde mwace osaleka kuphabe amitundu?