Habakkuk 1:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onani mitundu ya anthuyi, muipenyetsetse. Kudzakhala zododometsa ndipo mudzangoti kakasi. Pakuti ndidzachita zinthu zimene simudzakhulupirira mukadzazimva.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Penyani mwa amitundu, penyetsetsani, nimudabwe kwakukulu, pakuti ndichita ntchito masiku anu, imene simudzavomera chinkana akufotokozerani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Yangʼanani pakati pa mitundu ya anthu, ndipo penyetsetsani, ndipo muthedwe nazo nzeru. Pakuti ndidzachitadi zinthu pa nthawi yanu zimene inu simudzazikhulupirira, ngakhale wina atakufotokozerani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Penyani mwa amitundu, penyetsetsani, nimudabwe kwakukuru, pakuti ndicita nchito masiku anu, imene simudzabvomera cinkana akufotokozerani.