Habakkuk 1:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kulikonse kumene amapita, amachititsa mantha, amadzipangira okha malamulo, amadzipezera okha ulemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ali oopsa, achititsa mantha, chiweruzo chao ndi ukulu wao zituluka kwa iwo eni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwowa ndi anthu ochititsa mantha, ndipo ndi owopsa; amadzipangira okha malamulo ndi kudzipezera okha ulemu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ali oopsa, acititsa mantha, ciweruzo cao ndi ukulu wao zituruka kwa iwo eni.