Habakkuk 1:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Gulu lao lankhondo likubwera ndi nkhanza, anthu akuchita mantha iwo asanafike. Amagwira akapolo ochuluka ngati mchenga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzera chiwawa onsewo; nkhope zao zikhazikika zolunjika m'tsogolo; asonkhanitsa andende ngati mchenga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
onse akubwera atakonzekera zachiwawa. Gulu la ankhondo likubwera ngati mphepo ya mʼchipululu ndi kugwira akapolo ochuluka ngati mchenga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzera ciwawa onsewo; nkhope zao zikhazikika zolunjika m'tsogolo; asonkhanitsa andende ngati mcenga,