Habakkuk 2:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Udafuna kuwononga anthu a mitundu yambiri koma potero wachititsa manyazi banja lako, ndipo wataya moyo wako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wapangira nyumba yako chamanyazi, pakuononga mitundu yambiri ya anthu, ndipo wachimwira moyo wako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wakonzekera kuwononga mitundu yambiri ya anthu, kuchititsa manyazi nyumba yako yomwe ndi kuwononga moyo wako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wapangira nyumba yako camanyazi, pakuononga mitundu yambiri ya anthu, ndipo wacimwira moyo wako.