Habakkuk 2:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndi njerwa zomwe za nyumba yako zidzafuula chidzudzulo, ndipo mitanda idzathira mang'ombe ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mwala wa m'khoma ufuula, ndi mtanda wa kuphaso udzauvomereza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwala pa khoma udzafuwula, ndipo mitanda ya matabwa idzavomereza zimenezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mwala wa m'khoma upfuula, ndi mtanda wa kuphaso udzaubvomereza.