Habakkuk 2:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsoka kwa amene wamanga mzinda pokhetsa magazi, ndipo waukhazikitsa pozunza anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsoka iye wakumanga mudzi ndi mwazi, nakhazikitsa mudzi ndi chisalungamo!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsoka kwa amene amanga mzinda pokhetsa magazi ndi kukhazikitsa mzinda pochita zoyipa!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsoka tye wakumanga mudzindi mwazi, nakhazikitsa mudzi ndi cisalungamo!