Habakkuk 2:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero anthu onse adzazindikira ulemerero wa Chauta kuti ndi wodzaza, monga momwe madzi amadzazira nyanja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti dziko lapansi lidzadzazidwa ndi chidziwitso cha ulemerero wa Yehova, monga madzi amphimba pansi pa nyanja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti dziko lapansi lidzadzaza ndi chidziwitso cha ulemerero wa Yehova, monga momwe madzi amadzazira nyanja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti dziko lapansi lidzadzazidwa ndi cidziwitso ca ulemerero wa Yehova, monga madzi aphimba pansi panyanja.