Habakkuk 2:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsoka kwa amene amalemera ndi phindu lobera anzake, kuti akweze malo ake ndi kupewa zovuta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsoka iye wakupindulitsira nyumba yake phindu loipa, kuti aike chisanja chake ponyamuka, kuti alanditsidwe m'dzanja la choipa!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsoka kwa amene amalemera ndi chuma chochipeza mwachinyengo, kukweza malo ake okhalapo, kuthawa mavuto!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsoka iye wakupindulitsira nyumba yace phindu loipa, kuti aike cisanja cace ponyamuka, kuti alanditsidwe m'dzanja la coipa!