Habakkuk 3:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dzuŵa ndi mwezi zidangoti jega mu mlengalenga, zitaona kung'anipa kwa mivi yanu, ndi kunyezimira kwa mikondo yanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dzuwa ndi mwezi zinaima njera mokhala mwao; pa kuunika kwa mivi yanu popita iyo. Pa kung'anipa kwa nthungo yanu yonyezimira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzuwa ndi mwezi zinayima chilili mlengalenga, pa kungʼanima kwa mivi yanu yowulukayo, pa kunyezimira kwa mkondo wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dzuwa ndi mwezi zinaima njera mokhala mwao; Pa kuunika kwa mibvi yanu popita iyo. Pa kung'anipa kwa nthungo yanu yonyezimira.