Habakkuk 3:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudayendayenda m'dziko lapansi muli okwiya, mudapondereza anthu a mitundu yonse mwaukali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munaponda dziko ndi kulunda, munapuntha amitundu ndi mkwiyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munayendayenda mʼdziko lapansi muli ndi ukali, ndipo munapondereza mitundu ya anthu muli ndi mkwiyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munaponda dziko ndi kulunda, Munapuntha amitundu ndi mkwiyo.