Habakkuk 3:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
komabe kwanga nkukondwerera mwa Chauta, kwanga nkusangalala chifukwa cha Mulungu Mpulumutsi wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma ndidzakondwera mwa Yehova, ndidzasekerera mwa Mulungu wa chipulumutso changa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
komabe ine ndidzakondwera mwa Yehova, ndidzasangalala mwa Mulungu Mpulumutsi wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndidzakondwera mwa Yehova, Ndidzasekerera mwa Mulungu wa cipulumutso canga.