Habakkuk 3:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ambuye anga, Chauta, ndiwo amandipatsa mphamvu. Amalimbitsa miyendo yanga kuti ikhale ngati ya mbaŵala, kuti ndikafike mpaka pamwamba pa phiri. Kwa Woimbitsa nyimbo. Aimbire zazingwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova, Ambuye, ndiye mphamvu yanga, asanduliza mapazi anga ngati a mbawala, nadzandipondetsa pa misanje yanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ambuye Yehova ndiye mphamvu yanga; amalimbitsa miyendo yanga ngati ya mbawala yayikazi, amandithandiza kukafika pamwamba pa phiri. Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Pa zoyimbira za nsambo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova, Ambuye, ndiye mphamvuyanga, Asanduliza mapazi anga ngati a mbawala, Nadzandipondetsa pa misanje yanga.