Habakkuk 3:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaŵala ngati dzuŵa, kunyezimira kunkatuluka m'manja mwake, m'mene adabisamo mphamvu zake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi kunyezimira kwake kunanga kuunika; anali nayo mitsitsi ya dzuwa yotuluka m'dzanja lake, ndi komweko kunabisika mphamvu yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuwala kwa ulemerero wake kunali ngati kutuluka kwa dzuwa; kunyezimira kunkatuluka mʼdzanja lake, mʼmene anabisamo mphamvu zake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi kunyezimira kwace kunanga kuunika; Anali nayo mitsitsi ya dzuwa yoturuka m'dzanja lace. Ndi komweko kunabisika mphamvu yace.