Habakkuk 3:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidaona anthu a ku Kusani ali pa mavuto, nawonso a ku Midiyani adaagwedezeka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinaona mahema a Kusani ali mkusauka; nsalu zotchinga za dziko la Midiyani zinanjenjemera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinaona matenti a ku Kusani ali pa mavuto, mokhala a ku Midiyani muli ululu waukulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinaona mahema a Kusani ali mkusauka; Nsaru zocinga za dziko la Midyani zinanjenjemera.