Habakkuk 3:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, kodi mudaakwiyira mitsinje? Kodi mudaakalipira mifuleni? Kodi mudaazazira nyanja? Mutakwera pa akavalo anu mudapambanitsa anthu anu pa nkhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi Yehova anaipidwa nayo mitsinje? Mkwiyo wanu unali pamitsinje kodi, kapena ukali wanu panyanja, kuti munayenda pa akavalo anu, pa magaleta anu a chipulumutso?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Yehova, kodi munakwiyira mitsinje? Kodi munakalipira timitsinje? Kodi munapsera mtima nyanja pamene munakwera pa akavalo anu ndiponso magaleta anu achipulumutso?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi Yehova anaipidwa nayo mitsinje? Mkwiyo wanu unali pamitsinje kodi, Kapena ukali wanu panyanja, Kuti munayenda pa akavalo anu, Pa magareta anu a cipulumutso?