Habakkuk 3:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudasolola uta wanu m'chimake, ndipo mudatulutsa mivi m'phodo lake. Mudang'amba dziko lapansi ndi mitsinje.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munapombosola uta wanu; malumbiro analumbirira mafuko anali mau oona. Munang'amba dziko lapansi ndi mitsinje.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munasolola uta wanu mʼchimake, munayitanitsa mivi yambiri. Sela Munagawa dziko lapansi ndi mitsinje;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munapombosola uta wanu; Malumbiro analumbirira mafuko anali mau oona. Munang'amba dziko lapansi ndi mitsinje.