Haggai 2:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chaka chachiŵiri cha ufumu wa Dariusi, pa tsiku la 21, mwezi wachisanu ndi chiŵiri, Chauta adapatsa mneneri Hagai uthenga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwezi wachisanu ndi chiwiri, tsiku la makumi awiri ndi chimodzi la mweziwo, mau a Yehova anadza mwa Hagai mneneri, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku la 21 la mwezi wachisanu ndi chiwiri, Yehova anayankhula kudzera mwa mneneri Hagai kuti:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwezi wacisanu ndi ciwiri, tsiku la makumi awiri ndi cimodzi la mweziwo, mau a Yehova anadza mwa Hagai mneneri, ndi kuti,