Haggai 2:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chaka chachiŵiri cha ufumu wa Dariusi pa tsiku la 24 la mwezi wachisanu ndi chinai, Chauta adapatsa mneneri Hagai uthenga uwu wakuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku la makumi awiri ndi anai la mwezi wachisanu ndi chinai, chaka chachiwiri cha Dariusi, mau a Yehova anadza mwa Hagai mneneri, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chaka chachiwiri cha Dariyo, pa tsiku la 24 la mwezi wachisanu ndi chinayi, Yehova anayankhula ndi mneneri Hagai kuti:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku la makumi awiri ndi anai la mwezi wacisanu ndi cinai, caka caciwiri ca Dariyo, mau a Yehova anadza mwa Hagai mneneri, ndi kuti,