Haggai 2:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Zimene ndikunena Ine Chauta Wamphamvuzonse ndi izi: Mupemphe ansembe kuti agamule nkhani iyi:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atero Yehova wa makamu: Funsatu ansembe za chilamulo, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Yehova Wamphamvuzonse akuti, ‘Funsa ansembe za zimene lamulo likunena:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atero Yehova wa makamu: Funsatu ansembe za cilamulo, ndi kuti,