Haggai 2:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“ ‘Tsopano muganizire zimene zinkachitika asanayambe kumanganso Nyumba ya Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsono, samalirani, kuyambira lero ndi m'tsogolomo, kuti, kusanaikidwe mwala pa mwala m'Kachisi wa Yehova,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Tsopano muganizire zimenezi kuyambira lero mpaka mʼtsogolo. Ganizirani momwe zinthu zinalili asanayambe kumanga nyumba ya Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsono, samalirani, kuyambira lero ndi m'tsogolomo, kuti, kusanaikidwe mwala pa mwala m'Kacisi wa Yehova,