Haggai 2:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Lero ndi tsiku la 24, mwezi wachisanu ndi chinai, tsiku limene maziko a Nyumba ya Chauta aikidwa. Muganizirepo tsono,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musamalire, kuyambira lero ndi m'tsogolo, kuyambira tsiku la makumi awiri ndi chinai la mwezi wachisanu ndi chinai, kuyambira tsiku lija anamanga maziko a Kachisi wa Yehova, samalirani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
‘Kuyambira lero tsiku la 24 la mwezi wachisanu ndi chinayi mpaka mʼtsogolo, chonde ganizirani bwino tsiku limene munayika maziko a nyumba ya Yehova. Ganizirani bwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musamalire, kuyambira lero ndi m'tsogolo, kuyambira tsiku la makumi awiri ndi cinai la mwezi wacisanu ndi cinai, kuyambira tsiku lija anamanga maziko a Kacisi wa Yehova, samalirani.